Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+ Maliko 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno anawauza kuti: “Vinyoyu akuimira ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa+ chifukwa cha anthu ambiri.+
28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+
24 Ndiyeno anawauza kuti: “Vinyoyu akuimira ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa+ chifukwa cha anthu ambiri.+