Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+ 1 Timoteyo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anadzipereka kuti akhale dipo* lokwanira ndendende m’malo mwa onse.+ Zimenezi ndi zimene adzazichitire umboni pa nthawi zake. Tito 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iyeyo anadzipereka+ m’malo mwa ife kuti atilanditse+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse,+ kuti tikhale anthu akeake,+ odzipereka pa ntchito zabwino.+ Aheberi 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 n’chimodzimodzinso Khristu. Iye anaperekedwa nsembe kamodzi+ kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Ndipo nthawi yachiwiri+ imene adzaonekere+ sadzaonekera n’cholinga chochotsa uchimo.+ Anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse ndi amene adzamuone.+
28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+
6 Iye anadzipereka kuti akhale dipo* lokwanira ndendende m’malo mwa onse.+ Zimenezi ndi zimene adzazichitire umboni pa nthawi zake.
14 Iyeyo anadzipereka+ m’malo mwa ife kuti atilanditse+ ku moyo wochita zinthu zosamvera malamulo za mtundu uliwonse ndiponso kuti atiyeretse,+ kuti tikhale anthu akeake,+ odzipereka pa ntchito zabwino.+
28 n’chimodzimodzinso Khristu. Iye anaperekedwa nsembe kamodzi+ kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Ndipo nthawi yachiwiri+ imene adzaonekere+ sadzaonekera n’cholinga chochotsa uchimo.+ Anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse ndi amene adzamuone.+