Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+ Tito 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tizichita zimenezi pamene tikuyembekeza kukwaniritsidwa kwa chiyembekezo+ chosangalatsa ndi kuonetsedwa kwaulemerero+ kwa Mulungu wamkuluyo ndiponso kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu.
3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+
13 Tizichita zimenezi pamene tikuyembekeza kukwaniritsidwa kwa chiyembekezo+ chosangalatsa ndi kuonetsedwa kwaulemerero+ kwa Mulungu wamkuluyo ndiponso kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu.