Mateyu 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo. Mateyu 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+ Maliko 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti zinthu zonsezi zili m’nthawi yake yamapeto n’chiyani?”+ Luka 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti kwenikweni, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti zili pafupi kuchitika n’chiyani?”+
39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo.
20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+
4 “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti zinthu zonsezi zili m’nthawi yake yamapeto n’chiyani?”+
7 Pamenepo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti kwenikweni, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti zili pafupi kuchitika n’chiyani?”+