Habakuku 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anabwera kuchokera ku Temani, Woyerayo anabwera kuchokera kuphiri la Parana.+ [Seʹlah.]+ Ulemerero wake unaphimba kumwamba+ ndipo dziko lonse linamutamanda.+
3 Mulungu anabwera kuchokera ku Temani, Woyerayo anabwera kuchokera kuphiri la Parana.+ [Seʹlah.]+ Ulemerero wake unaphimba kumwamba+ ndipo dziko lonse linamutamanda.+