Mateyu 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+ Mateyu 24:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pakuti monga mmene analili masiku a Nowa,+ ndi mmenenso kukhalapo kwa Mwana wa munthu kudzakhalire.+ Mateyu 24:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anthu ananyalanyaza zimene zinali kuchitika mpaka chigumula chinafika n’kuwaseseratu onsewo.+ Zidzateronso ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.
27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+
37 Pakuti monga mmene analili masiku a Nowa,+ ndi mmenenso kukhalapo kwa Mwana wa munthu kudzakhalire.+
39 Anthu ananyalanyaza zimene zinali kuchitika mpaka chigumula chinafika n’kuwaseseratu onsewo.+ Zidzateronso ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.