Mateyu 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+ Luka 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso, monga zinachitikira m’masiku a Nowa,+ zidzachitikanso chimodzimodzi m’masiku a Mwana wa munthu.+
27 Pakuti mmene mphezi+ imang’animira kuchokera kum’mawa, ndi kuwala mpaka kumadzulo, zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.+
26 Komanso, monga zinachitikira m’masiku a Nowa,+ zidzachitikanso chimodzimodzi m’masiku a Mwana wa munthu.+