Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 107:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo,+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+ Yona 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+
13 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo,+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+
2 kuti:“Pamene ndinali m’masautso ndinaitana Yehova,+ ndipo anandiyankha.+Ndinafuula kupempha thandizo ndili m’Manda* akuya.+Ndipo inu munamva mawu anga.+