Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+

  • Oweruza 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho Aisiraeli anasautsika kwadzaoneni chifukwa cha Amidiyani. Pamenepo, ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+

  • Oweruza 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani+ inu Mulungu wathu, chifukwa takusiyani ndipo tikutumikira Abaala.”+

  • 2 Mbiri 33:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena