2 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova wanena kuti, ‘Taona, ndikukugwetsera tsoka m’nyumba yako yomwe.+ Ndidzatenga akazi ako iwe ukuona ndi kuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi ako anthu onse akuona.+ Salimo 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu anu mwawaonetsa zovuta.+Mwatimwetsa vinyo ndipo tikuyenda dzandidzandi.+ Salimo 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwachititsa munthu wamba kutipondaponda.+Tadutsa pamoto ndi pamadzi,+Ndipo inu mwatipatsa mpumulo.+ Salimo 88:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwandiika m’dzenje lakuya kwambiri,M’malo a mdima, m’phompho lalikulu.+
11 Ndiyeno Yehova wanena kuti, ‘Taona, ndikukugwetsera tsoka m’nyumba yako yomwe.+ Ndidzatenga akazi ako iwe ukuona ndi kuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi ako anthu onse akuona.+
12 Mwachititsa munthu wamba kutipondaponda.+Tadutsa pamoto ndi pamadzi,+Ndipo inu mwatipatsa mpumulo.+