-
2 Samueli 12:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Davide ataona kuti atumiki ake akunong’onezana, anazindikira kuti mwana uja wamwalira. Choncho anafunsa atumiki akewo kuti: “Kodi mwana uja wamwalira?” Iwo anamuyankha kuti: “Inde wamwalira.”
-
-
2 Samueli 15:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Nthawi yomweyo, Davide anauza atumiki ake onse amene anali naye limodzi mu Yerusalemu, kuti: “Nyamukani, tiyeni tithawe,+ pakuti sipapezeka munthu wopulumuka m’manja mwa Abisalomu. Chitani changu, pakuti mwina angafike mofulumira ndi kutipeza n’kutichitira choipa komanso kukantha mzinda ndi lupanga!”+
-