Salimo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+ Yona 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene munandiponya m’malo ozama, pansi penipeni pa nyanja yakuya,+Madzi amphamvu anandimiza.Mafunde anu amphamvu anadutsa pamwamba panga.+
6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+
3 Pamene munandiponya m’malo ozama, pansi penipeni pa nyanja yakuya,+Madzi amphamvu anandimiza.Mafunde anu amphamvu anadutsa pamwamba panga.+