Salimo 69:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndinali kupemphera kwa inu Yehova,+Pa nthawi yovomerezedwa, inu Mulungu.+Ndiyankheni mwa kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha, ndipo sonyezani kuti ndinudi mpulumutsi.+ Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+
13 Koma ine ndinali kupemphera kwa inu Yehova,+Pa nthawi yovomerezedwa, inu Mulungu.+Ndiyankheni mwa kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha, ndipo sonyezani kuti ndinudi mpulumutsi.+