Genesis 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anayamba kulota.+ M’malotowo anaona makwerero ochokera pansi mpaka kumwamba. Angelo a Mulungu anali kukwera ndi kutsika pamakwereropo.+ Chivumbulutso 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako mbonizo zinamva mawu ofuula+ ochokera kumwamba akuziuza kuti: “Kwerani kuno.”+ Ndipo zinakwera kumwamba mumtambo, moti adani awo anaziona.
12 Kenako anayamba kulota.+ M’malotowo anaona makwerero ochokera pansi mpaka kumwamba. Angelo a Mulungu anali kukwera ndi kutsika pamakwereropo.+
12 Kenako mbonizo zinamva mawu ofuula+ ochokera kumwamba akuziuza kuti: “Kwerani kuno.”+ Ndipo zinakwera kumwamba mumtambo, moti adani awo anaziona.