Salimo 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Sonkhanitsani okhulupirika anga kwa ine,+Amene achita pangano mwa kupereka nsembe.”+ Salimo 147:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova akumanga Yerusalemu.+Anthu okhala mu Isiraeli amene anabalalika akuwasonkhanitsanso pamodzi.+ Chivumbulutso 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khomo lotseguka kumwamba. Ndipo mawu oyamba amene ndinawamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga.+ Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno,+ ndikuonetse zinthu zimene ziyenera kuchitika.”+
2 Yehova akumanga Yerusalemu.+Anthu okhala mu Isiraeli amene anabalalika akuwasonkhanitsanso pamodzi.+
4 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khomo lotseguka kumwamba. Ndipo mawu oyamba amene ndinawamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga.+ Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno,+ ndikuonetse zinthu zimene ziyenera kuchitika.”+