Ezekieli 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakati pa motowo panali zinazake zooneka ngati zamoyo zinayi,+ ndipo zamoyozo zinali zooneka ngati anthu. Chivumbulutso 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nthawi zonse zamoyozo zikamapereka ulemerero, ndi ulemu, ndiponso zikamayamikira+ Wokhala pampando wachifumuyo,+ Iye amene adzakhalabe ndi moyo kwamuyaya,+
5 Pakati pa motowo panali zinazake zooneka ngati zamoyo zinayi,+ ndipo zamoyozo zinali zooneka ngati anthu.
9 Nthawi zonse zamoyozo zikamapereka ulemerero, ndi ulemu, ndiponso zikamayamikira+ Wokhala pampando wachifumuyo,+ Iye amene adzakhalabe ndi moyo kwamuyaya,+