Miyambo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maso a Yehova ali paliponse.+ Amayang’ana anthu oipa ndi abwino omwe.+ Ezekieli 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Malimu a mawilowo anali aatali kwambiri moti anali ochititsa mantha. Malimu anayi onsewo anali odzaza ndi maso.+ Ezekieli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zamoyozo zinali ndi maso paliponse. Zinali ndi maso pamatupi awo, kumbuyo kwawo, m’manja awo, m’mapiko awo, ndiponso kuzungulira mawilo onse.+ Pambali pa kerubi aliyense mwa akerubi anayi amenewo, panali wilo. Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
18 Malimu a mawilowo anali aatali kwambiri moti anali ochititsa mantha. Malimu anayi onsewo anali odzaza ndi maso.+
12 Zamoyozo zinali ndi maso paliponse. Zinali ndi maso pamatupi awo, kumbuyo kwawo, m’manja awo, m’mapiko awo, ndiponso kuzungulira mawilo onse.+ Pambali pa kerubi aliyense mwa akerubi anayi amenewo, panali wilo.
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+