Yesaya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.” Luka 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Chifukwa Wamphamvuyo wandichitira zazikulu, ndipo dzina lake ndi loyera.+
3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.”