-
Levitiko 23:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pa tsiku loweyulira mtolo wanu uku ndi uku, muzipereka mwana wa nkhosa wopanda chilema, wosapitirira chaka chimodzi, kuti akhale nsembe yopsereza yoperekedwa kwa Yehova.
-