1 Yohane 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene Yesu Khristu ankabwera panali madzi komanso magazi. Sikuti panali madzi okha,+ koma panalinso magazi.+ Ndipo mzimu woyera ukuchitira umboni zimenezi,+ chifukwa mzimuwo umabweretsa choonadi poyera. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, ptsa. 27-282/1/1987, ptsa. 16-17
6 Pamene Yesu Khristu ankabwera panali madzi komanso magazi. Sikuti panali madzi okha,+ koma panalinso magazi.+ Ndipo mzimu woyera ukuchitira umboni zimenezi,+ chifukwa mzimuwo umabweretsa choonadi poyera.