Machitidwe 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Muzidziyangʼanira nokha+ komanso kusamalira gulu lonse la nkhosa, limene mzimu woyera wakuikani kuti muziliyangʼanira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi a Mwana wake weniweni.+ Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa mwana wakeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi ake,+ inde, takhululukidwa machimo athu,+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwake kwakukulu. 1 Petulo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali+ a Khristu,+ omwe ndi ofanana ndi magazi a nkhosa yopanda chilema komanso yopanda mawanga.+
28 Muzidziyangʼanira nokha+ komanso kusamalira gulu lonse la nkhosa, limene mzimu woyera wakuikani kuti muziliyangʼanira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi a Mwana wake weniweni.+
7 Kudzera mwa mwana wakeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi ake,+ inde, takhululukidwa machimo athu,+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.
19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali+ a Khristu,+ omwe ndi ofanana ndi magazi a nkhosa yopanda chilema komanso yopanda mawanga.+