1 Yohane 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ameneyu ndi Yesu Khristu, amene anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi. Sanabwere kudzera mwa madzi+ okha, koma anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi.+ Ndipo mzimu+ ndi umene ukuchitira umboni, chifukwa mzimu ndiwo choonadi. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, ptsa. 27-282/1/1987, ptsa. 16-17
6 Ameneyu ndi Yesu Khristu, amene anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi. Sanabwere kudzera mwa madzi+ okha, koma anabwera kudzera mwa madzi ndi magazi.+ Ndipo mzimu+ ndi umene ukuchitira umboni, chifukwa mzimu ndiwo choonadi.