Salimo 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti ndinali kulankhula za cholakwa changa.+Ndipo ndinali kudera nkhawa za tchimo langa.+ Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+ 1 Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, chotero tikavomereza machimo athu,+ adzatikhululukira ndi kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+
4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+
9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, chotero tikavomereza machimo athu,+ adzatikhululukira ndi kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+