Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 86:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+

      Kukoma mtima kosatha kumene mumawasonyeza onse oitana pa inu ndi kwakukulu.+

  • Salimo 103:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+

      Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+

  • Yesaya 44:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+

  • Hoseya 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Bwerera kwa Yehova ndi mawu osonyeza kulapa.+ Anthu nonsenu uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zabwino zochokera kwa ife, ndipo mawu apakamwa pathu akhale ngati ana amphongo a ng’ombe amene tikuwapereka nsembe kwa inu.+

  • Luka 7:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuza kuti, machimo ake akhululukidwa,+ ngakhale kuti ndi ochuluka. N’chifukwa chake akusonyeza chikondi chochuluka. Koma amene wakhululukidwa machimo ochepa amasonyezanso chikondi chochepa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena