Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+

      Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+

  • Yesaya 43:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Ineyo ndi amene ndikufafaniza+ zolakwa zako,+ ndipo machimo ako sindidzawakumbukiranso.+

  • Yesaya 44:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+

  • Luka 7:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Atasowa chopereka kuti abweze ngongolezo, mwiniwake uja anakhululukira+ onsewo ndi mtima wonse. Kodi ndani mwa awiriwo amene angam’konde kwambiri?”

  • 1 Timoteyo 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ndinalandira kukoma mtima kwakukulu+ kwa Ambuye wathu. Ndinalandiranso chikhulupiriro ndi chikondi chodzera mwa Khristu Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena