-
1 Timoteyo 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ndinalandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu Ambuye wathu. Ndinalandiranso chikhulupiriro ndi chikondi cha Khristu Yesu.
-