1 Timoteyo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ndinalandira kukoma mtima kwakukulu+ kwa Ambuye wathu. Ndinalandiranso chikhulupiriro ndi chikondi chodzera mwa Khristu Yesu.+
14 Koma ndinalandira kukoma mtima kwakukulu+ kwa Ambuye wathu. Ndinalandiranso chikhulupiriro ndi chikondi chodzera mwa Khristu Yesu.+