Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Wodala ndi munthu amene wakhululukidwa zolakwa zake, amene machimo ake aphimbidwa.+

  • Salimo 103:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+

      Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+

  • Yesaya 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova akuti, “Bwerani tsopano anthu inu. Tiyeni tikambirane ndipo ine ndikuthandizani kuti mukhalenso pa ubwenzi wabwino ndi ine.+ Ngakhale machimo anu atakhala ofiira kwambiri, adzayera kwambiri.+ Ngakhale atakhala ofiira ngati magazi, adzayera ngati thonje.

  • Mateyu 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Izi zinamvetsa chisoni mbuyeyo ndipo anamusiya kapoloyo+ ndi kumukhululukira ngongole yake ija.+

  • Luka 7:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuza kuti, machimo ake akhululukidwa,+ ngakhale kuti ndi ochuluka. N’chifukwa chake akusonyeza chikondi chochuluka. Koma amene wakhululukidwa machimo ochepa amasonyezanso chikondi chochepa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena