Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndiyeretseni ndi hisope ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+

      Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa chipale chofewa.+

  • Yesaya 44:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+

  • Maliro 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.

      Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+

  • Mika 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena