Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 wansembe azim’lamula kuti atenge zofunika pa kudziyeretsa kwake. Azitenga mbalame zamoyo ziwiri zosadetsedwa,+ nthambi ya mtengo wa mkungudza,+ ulusi wofiira kwambiri+ ndi kamtengo ka hisope.+

  • Numeri 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno munthu wosadetsedwa+ atenge kamtengo ka hisope.+ Akaviike m’madziwo n’kuwaza hemalo. Awazenso ziwiya zonse ndi anthu onse amene anali muhemalo. Komanso, awaze munthu amene anakhudza fupa la munthu, kapena kukhudza munthu wophedwa, kapenanso mtembo uliwonse, ngakhalenso manda a munthu.

  • Aheberi 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena