1 Akorinto 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+ Aheberi 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, pamene tasiya chiphunzitso choyambirira+ cha Khristu+ tsopano, tiyeni tiyesetse mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+ Tisayambe kuyalanso maziko,+ amene ndi kulapa ntchito zakufa,+ chikhulupiriro mwa Mulungu,+
11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+
6 Pa chifukwa chimenechi, pamene tasiya chiphunzitso choyambirira+ cha Khristu+ tsopano, tiyeni tiyesetse mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+ Tisayambe kuyalanso maziko,+ amene ndi kulapa ntchito zakufa,+ chikhulupiriro mwa Mulungu,+