1 Mafumu 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Popeza wadzichepetsa chifukwa cha ine, sindidzabweretsa tsokali m’masiku ake.+ M’malomwake, ndidzalibweretsa panyumba yake m’masiku a mwana wake.”+ Yoweli 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndani akudziwa kuti mwina adzasintha maganizo ake ndi kukumverani chisoni+ ndipo kenako adzakusiyirani madalitso,+ nsembe yambewu ndi nsembe yachakumwa kuti mupereke kwa Yehova Mulungu wanu? Yona 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mulungu woona anaona ntchito zawo.+ Anaona kuti alapa ndi kusiya njira zawo zoipa.+ Choncho, Mulungu woona anasintha maganizo ake+ pa tsoka limene ananena kuti awabweretsera, moti sanawabweretsere.+
29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Popeza wadzichepetsa chifukwa cha ine, sindidzabweretsa tsokali m’masiku ake.+ M’malomwake, ndidzalibweretsa panyumba yake m’masiku a mwana wake.”+
14 Ndani akudziwa kuti mwina adzasintha maganizo ake ndi kukumverani chisoni+ ndipo kenako adzakusiyirani madalitso,+ nsembe yambewu ndi nsembe yachakumwa kuti mupereke kwa Yehova Mulungu wanu?
10 Ndiyeno Mulungu woona anaona ntchito zawo.+ Anaona kuti alapa ndi kusiya njira zawo zoipa.+ Choncho, Mulungu woona anasintha maganizo ake+ pa tsoka limene ananena kuti awabweretsera, moti sanawabweretsere.+