Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Patuka pa choipa ndipo uchite chabwino,+

      Ukatero udzakhala padziko lapansi mpaka kalekale.+

  • Miyambo 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chuma cha anthu oipa chidzakhala chopanda phindu,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+

  • Miyambo 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+

  • Habakuku 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Taona! Iye wadzitukumula+ ndipo si wowongoka mtima. Koma wolungama adzakhalabe ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.+

  • Aroma 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira monga mfumu pamodzi ndi imfa,+ momwemonso kukoma mtima kwakukulu+ kulamulire monga mfumu kudzera m’chilungamo. Zimenezi zichitike kuti moyo wosatha+ ubwere kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.

  • 1 Petulo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti “amene akufuna kusangalala ndi moyo ndi kuona masiku abwino,+ aletse lilime+ lake kuti lisalankhule zoipa ndi milomo yake kuti isalankhule chinyengo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena