Salimo 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tetezani lilime lanu ku zinthu zoipa,+Ndi milomo yanu kuti isalankhule chinyengo.+ 1 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+
11 Nawonso amayi akhale opanda chibwana, osati amiseche.+ Akhale ochita zinthu mosapitirira malire,+ ndi okhulupirika m’zinthu zonse.+