Mateyu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+ Luka 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+
4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+
42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+