Aefeso 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+ 1 Atesalonika 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 osati mwa chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ ngati chimene anthu a mitundu ina+ osadziwa Mulungu+ ali nacho.
12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+
5 osati mwa chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ ngati chimene anthu a mitundu ina+ osadziwa Mulungu+ ali nacho.