Yuda 21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse Mulungu kukukondani.+ Chitani zimenezi pamene mukuyembekezera kuti chifundo+ cha Ambuye wathu Yesu Khristu chidzakutsegulireni njira yoti mulandirire moyo wosatha.+
21 pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse Mulungu kukukondani.+ Chitani zimenezi pamene mukuyembekezera kuti chifundo+ cha Ambuye wathu Yesu Khristu chidzakutsegulireni njira yoti mulandirire moyo wosatha.+