Ezara 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima polola anthu ena kuti apulumuke ndipo watipatsa malo otetezeka* mʼmalo ake oyera+ kuti maso athu awale. Mulungu wathu watitsitsimula pangʼono mu ukapolo wathu.
8 Koma kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima polola anthu ena kuti apulumuke ndipo watipatsa malo otetezeka* mʼmalo ake oyera+ kuti maso athu awale. Mulungu wathu watitsitsimula pangʼono mu ukapolo wathu.