Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zimenezi zinam’vutitsa maganizo kwambiri Davide+ chifukwanso anthu anali kukambirana zom’ponya miyala.+ Anthuwo anali kukambirana zimenezi chifukwa aliyense wa iwo anali wokwiya kwambiri+ poona zimene zachitikira ana awo aamuna ndi ana awo aakazi. Choncho, Davide anadzilimbitsa mwa Yehova Mulungu wake.+

  • Salimo 56:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ine ndidzadalira inu, tsiku lililonse limene ndingachite mantha.+

  • Salimo 68:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+

      Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+

      Mulungu adalitsike.+

  • Salimo 138:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pa tsiku limene ine ndinaitana, inu munandiyankha.+

      Munandilimbitsa mtima ndi kundipatsa mphamvu.+

  • Yesaya 41:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena