Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo ana a Dani anamuuza kuti: “Usayandikire kuno ndipo tisamvenso mawu akowo, chifukwa anthu olusa+ angakupwetekeni, ndipo iweyo ungataye moyo wako ndi kutayitsa moyo wa anthu a m’nyumba yako.”

  • 1 Samueli 22:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Amuna onse amene anali kusautsidwa,+ onse amene anali ndi ngongole,+ ndi onse amene anali ndi zodandaula+ anayamba kusonkhana kwa iye,+ ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo.+ Anthu onse amene anali naye anakwana 400.

  • 2 Samueli 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Husai anapitiriza kunena kuti: “Iwe ukuwadziwa bwino bambo wako ndi amuna amene ali nawo kuti iwo ndi amphamvu+ ndipo mitima ikuwapweteka+ ngati chimbalangondo chimene chataya ana ake kuthengo.+ Ukudziwanso bwino kuti bambo wako ndi munthu wankhondo+ ndipo sangagone kumene kuli anthu.

  • 2 Mafumu 4:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mayiyo atafika kwa munthu wa Mulungu woona paphiripo, nthawi yomweyo anam’gwira mapazi.+ Gehazi ataona zimenezo, anabwera pafupi kuti am’kankhe mayiyo.+ Koma munthu wa Mulungu woonayo+ anamuuza kuti: “Musiye,+ mtima wake ukum’pweteka kwambiri.+ Koma Yehova wandibisira,+ sanandiuze.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena