2 Mafumu 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Patapita nthawi, mayiyo anauza mwamuna wake+ kuti: “Tsopano ndikudziwa kuti munthu amene amadzera kuno nthawi zonse uja, ndi munthu woyera wa Mulungu.+
9 Patapita nthawi, mayiyo anauza mwamuna wake+ kuti: “Tsopano ndikudziwa kuti munthu amene amadzera kuno nthawi zonse uja, ndi munthu woyera wa Mulungu.+