2 Mafumu 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo atangowoloka, Eliya anauza Elisa kuti: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikuchitire ndisanakuchokere.”+ Elisa anati: “Chonde, magawo awiri+ a mzimu+ wanu abwere kwa ine.”+
9 Iwo atangowoloka, Eliya anauza Elisa kuti: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikuchitire ndisanakuchokere.”+ Elisa anati: “Chonde, magawo awiri+ a mzimu+ wanu abwere kwa ine.”+