Luka 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamene anali kuwadalitsa choncho, analekana nawo, ndi kuyamba kukwera kumwamba.+ Aheberi 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano, palibe angatsutse kuti wamng’ono amadalitsidwa ndi wamkulu.+