Miyambo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtima wa mwamuna wake* umamudalira, ndipo mwamunayo sasowa kalikonse.+ 1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+