-
Mateyu 18:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Pamenepo kapoloyu anagwada pansi ndi kuyamba kumuweramira n’kunena kuti, ‘Ndilezereniko mtima chonde, ndidzakubwezerani zonse.’
-