Yobu 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinkawasankhira njira, ndipo ndinkakhala pansi patsogolo pawo.Ndinali ngati mfumu pakati pa asilikali ake,+Ndiponso ngati wotonthoza olira.+ 2 Akorinto 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse,+ kuti tithe kutonthoza+ amene ali m’masautso amtundu uliwonse, chifukwa nafenso tatonthozedwa ndi Mulungu.+ 1 Atesalonika 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho pitirizani kutonthozana ndi kulimbikitsana+ monga mmene mukuchitira.+
25 Ndinkawasankhira njira, ndipo ndinkakhala pansi patsogolo pawo.Ndinali ngati mfumu pakati pa asilikali ake,+Ndiponso ngati wotonthoza olira.+
4 amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse,+ kuti tithe kutonthoza+ amene ali m’masautso amtundu uliwonse, chifukwa nafenso tatonthozedwa ndi Mulungu.+