Aroma 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+ 2 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,
4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+
16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,