Yesaya 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu inu limbitsani manja ofooka ndiponso mawondo agwedegwede.+ Aroma 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kapena kuti tidzalimbikitsane+ mwa chikhulupiriro, chanu ndi changa.+ Aroma 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aliyense wa ife azikondweretsa mnzake pa zinthu zabwino zomulimbikitsa.+