Genesis 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yehova anati: “Kodi ndingamubisire Abulahamu zimene ndikufuna kuchita?+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+