Miyambo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+ Miyambo 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtima wosangalala ndiwo mankhwala ochiritsa,+ koma mtima wosweka umaumitsa mafupa.+
13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+